Ofesi ya zaumoyo m’boma la Zomba yapempha mafumu kuti awonetsetsese kuti anthu awo akhale ndi zimbudzi pofuna kupewa kolera. Wofalitsa nkhani ku ofesi yadza umoyo Boma la Zomba Arnold Mndalira ndiyemwe wayankhula izi ku Zomba pa msonkhano wa atolankhani omwe adakonza pofuna kudziwitsa olemba nkhani momwe kampeni ya “Tithetse Kolera” ikuyendera m’bomali. Mndalira adati mamfumu […]
The post Ofesi ya zaumoyo yapempha anthu kuti akhale ndi zimbudzi pofuna kupewa kolera appeared first on Malawi 24.