Anthu atali atali amakhala pachiopsezo ku mphenzi, watelo katswiri wazanyengo

A Akimu Phiri, m’modzi wa katswiri ku nthambi yoona za nyengo m’dziko lino, achenjeza anthu omwe ndi atali atali kuti akuyenera kumayenda mosamala maka munyengo ya mvula ponena akuti anthuwa amakhala pa chiopsezo chowombedwa ndi mphenzi. A Phiri anati anthu omwe ndi atali atali amakhala pa chiopsezo akamayenda pa malo oti palibe mitengo kapena zinthu […]

The post Anthu atali atali amakhala pachiopsezo ku mphenzi, watelo katswiri wazanyengo appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください