Azibambo atatu onyenga! UNISA yawakana a Pemphero Mphande, a Karim ndi a Namadingo

Kaya mwina pano tiziti Mr anavaya, kapena chabe kuti atate anavaya? Chifukwa ati za doc anavaya zija ndi za ukapilikoni basi. Utambwali wa masanasana. Komanso pali nkhawa pang’ono kuti kodi nkhani amalemba Mr P, hiii pepani Dr P, ndi zoona kapena nazonso ndi zabodza? Chifukwa a sukulu ya ukachenjede ya ku Sasa Afrika ya UNISA […]

The post Azibambo atatu onyenga! UNISA yawakana a Pemphero Mphande, a Karim ndi a Namadingo appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください