Zikuoneka kuti madobadoba aku Nigeria komaso matsotsi aku South Africa athira mchenga mumpunga wagulu pomwe awonetsa Pemphero Mphande ndi Patience Namadingo chidameta nkhanga mpala powapatsa ma digili awulemu abodza. Chatsitsa dzaye nchakuti kuyambira lamulungu sabata ino, dzina la Pemphero Mphande linali posepose pomwe anauza mtundu wa a Malawi kuti atha kumatchedwano dokotala kamba koti sukulu […]
The post U-Doc uja wapita basi? UNISA yati siinapeleke madigili aulemu kwa Namadingo, Mphande appeared first on Malawi 24.