Apolisi mu mzinda wa Lilongwe akusaka dalaivala wa truck Grey Chisinga yemwe akuti analanda mfuti ya wapolisi wina pa nthawi imene apolisi anamanga dailavayu pa mlandu ozembetsa feteleza. Wachiwiri kwa mneneri wapolisi ku Central West Region Police, a Foster Benjamin, ati a Chisinga akuganiziridwa kuti anagulitsa feteleza opyola matumba 600 yemwe adanyamula kuchoka ku Blantyre […]
The post Apolisi akusakasaka dalaivala yemwe analanda mfuti ya wapolisi appeared first on Malawi 24.