Bus ya Mzuni yachita ngozi lero

Bus ya pa Mzuzu University yomwe nambala yake ndi  MZ10315 yachita ngozi pa Kanduli m’mawa uno pamene ophunzira a sukulu ya ukachenjedeyi anali pa ulendo opita m’boma la Nkhata-Bay. M’modzi mwa ophunzira amene anali nawo pa ulendowu  anauza Malawi24 kuti zikuonetsa kuti ngoziyi yachitika kamba kakuti Bus yo inaduka mabuleki. Pakadali pano omwe avulala athamangira […]

The post Bus ya Mzuni yachita ngozi lero appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください