Mkulu wa pulogalamu yoona za matenda a chifuwa chachikulu mdziko muno a Dr James Mpunga ayamikira achinyamata powonetsa luso lawo mu chikho cha ndalama zokwana 5 Million Kwacha cha sukulu za sekondale zomwe zikupezeka mdera lapakati mu mzinda wa Zomba ndipo ati ndikofunika kupereka mwayi kwa anyamatawa kuti adzathe kusewera matimu akuluakulu. Masewero otsiliza a […]
The post Dokotala wayamikira achinyamata ku Zomba powonetsa luso lawo appeared first on Malawi 24.