Wapolisi wayimitsidwa ntchito kamba ka kilipi yotchula Kunkuyu

Apolisi m’dziko muno ayimitsa pa ntchito wapolisi nzawo a Inspector Susan Kachinga omwe akukhudzidwa ndi kilipi yomwe a Moses Kunkuyu anatchulidwamo kuti akukhudzidwa ndi kuphedwa kwa Allan Wittika. Sabata yatha, apolisi anamanga Inspector Kachinga komanso a Mercy Chiligo ndi Chipiriro Kalima powaganizira kuti ndi amene akufalitsa nkhani zabodza zokhudza kafukufuku amene akuchitika kutsatila kuphedwa kwa […]

The post Wapolisi wayimitsidwa ntchito kamba ka kilipi yotchula Kunkuyu appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください