Mfumu yaikulu Kachenga ya m’boma la Balaka yamwalira. Bwanamkubwa wa boma la Balaka a Tamanya Harawa ndiwo atsimikiza izi mu kalata yomwe asainira. A Harawa ati mfumu Kachenga yamwalira lero masana akulandira chithandizo cha mankhwala pa chipatala cha Zomba Central. Mwambo oika m’manda thupi la malemu Kachenga, omwe dzina lawo ndi Mary Saidi, ulengezedwabe. Anabadwa […]
The post Mfumu yaikulu Kachenga yamwalira appeared first on Malawi 24.