Ofalitsa nkhani za Polisi ya Balaka, a Inspector Gladson M’bumpha, ati apolisi anjata anthu 18 omwe ndi kuphatikizapo amai atatu komanso mphongo 15 powaganizira kuti amaba mafuta mu sitima ya panjanji. Malingana ndi a M’bumpha, oganizilidwawa adamangidwa m’bandakucha wa loweluka pa 28 October, 2023 m’mudzi mwa Kanono, mfumu yaikulu Symon m’boma la Neno. A M’bumpha […]
The post Amai atatu komanso abambo 15 anjatidwa powaganizira kuti amaba mafuta mu sitima appeared first on Malawi 24.