Bambo wina wa zaka 37 yemwe amalandira thandizo la mankhwala pa chipatala cha Mzuzu Central wadzipha podzimangilira m’chimbudzi cha pa chipatalapo. Watsimikiza za nkhaniyi ndi oyankhulira chipatala cha Mzuzu Central a Anord Kayira omwe azindikira malemuwa ngati a Nowa Tembo omwe adzikhweza usiku wa lachinayi pa 26 October, 2023. A Kayira ati malemu Tembo anafika […]
The post Odwala wadzikhwezera muchimbudzi cha pachipatala appeared first on Malawi 24.