Kwa Goliati m’boma la Thyolo, anthu atatu afa ndipo m’modzi wapulumuka pomwe amafuna kupitiliza kukumba chitsimwe chomwe anayatsamo tayala la galimoto kuti aphwanye thanthwe lomwe analipeza. Watsimikiza za nkhaniyi ndi ofalitsa nkhani wa apolisi m’chigawo cha kummwera cha kummawa a Edward Kabango omwe ati ngoziyi yachitika lachinayi pa 26 October, 2023. A Kabango awuza nyumba […]
The post Anthu atatu afera m’chitsime chomwe amakumba appeared first on Malawi 24.