…wati nduna zachimuna zambiri ndi “zigandanga” Oyimba Jolly Bro yemwe ali m’dziko la America, waopseza kuti abwera ku Malawi kuno chaka cha mawa kudzathana ndi nduna zina zomwe akuti ndi zoyipa kuphatikizaso anthu omwe anapha Allan Wittika. Izi ndi malingana ndi kanema yemwe Alberto Fernando Zacharias otchedwaso JB anajambula layivi (live) pa tsamba lake la […]
The post “Ndikubwera ku Malawi-ko kudzapha anthu oyipa” – watelo JB appeared first on Malawi 24.