Zeze sanandilande Dorothy Shonga – watelo Blakjak

Oyimba nyimbo za dancehall Blakjak wakanitsitsa mwa ntu wa galu mphekesera zomwe zakhala zikumveka zoti analandidwa Dorothy Shonga ndi Zeze Kingstone Blakjak yemwe anabadwa Fatsani Che Kalonda amayankhula izi pomwe amacheza ndi kanema ina ya nsangulutso pa masamba anchezo sabata yatha. Mkati mwa kucheza, Blakjak anatsindika kuti iye ndi Dorothy Shonga anali pa chinzake chabe […]

The post Zeze sanandilande Dorothy Shonga – watelo Blakjak appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください