Nkokenkoke ku bwalo la milandu ku Chiradzulu

Kunali mkokekoke ndi maphokoso ochuluka kuchokera  kwa otsatila oganizilidwa milandu pamene oweruza milandu ku Chiradzulu anakana kupereka belo kwa anthu 15 omwe akuzengedwa milandu yakuba ndi kuononga katundu wa esiteti ya Mulli. Anthuwa adandaula kuti oweruza milanduyi yemwe dzina lake ndi Smart Maluwasa wakana kupeleka belo ngakhale kuti mboni zaboma zopitilira zitatu zati zikuzindikilapo anthu awiri […]

The post Nkokenkoke ku bwalo la milandu ku Chiradzulu appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください