…chikwangwani cha polisi chikufunika K350,000 Nkhonya yobwezera kuwawa; ophunzira pa sukulu ya ukachenjede ya Mzuni nkhawa ili bii pomwe za dziwika kuti ndalama yokwana K93 miliyoni ndi yomwe ifunike pa ntchito yobwezeretsa zinthu zomwe zinawonongeka pa ziwonetsero mwezi watha. Pa 15 September chaka chino, ophunzira pa sukuluyi anachita ziwonetsero atakanika kuvana chichewa ndi akuluakulu oyendetsa […]
The post Ka peanut? K93 miliyoni ikufunika yokozera zomwe ophunzira pa Mzuni anawononga appeared first on Malawi 24.