Ngati a Peter Mutharika amayesa kuti akadutsa moyela ku convention yawo, apa ndiye aganize kawiri. A Kondwani Nankhumwa sali mocheza ndipo ati akawaswa a Mutharika. Malinga ndi wailesi ya Zodiak, a Nankhumwa ati iwo sabwelera pambuyo ndi lingaliro lawo lofuna kutenga chipani cha DPP ndinso dziko lino mu 2025. A Nankhumwa amene ndi mtsogoleri wa […]
The post Muuzeni Mutharika’yo aime ndimuthibule bwino – watero Nankhumwa appeared first on Malawi 24.