Kusamvana kunabuka pamalo omwetsera mafuta

Kusamvana kunabuka lero m’mawa uno pamalo ena omwetsera mafuta a Petroda pa Kamuzu Road m’boma la Salima pamene mkulu wina amakana kusuntha galimoto lake. Mkulu wina yemwe amaonetsetsa kuti zinthu zikuyenda mwa dongosolo anapempha bwana wina kuti asunthe kaye galimoto lake, kuti ena apeze mpata odutsa kamba kakuti adayima poti mzake atha kutulukira ukira. Bwanayo […]

The post Kusamvana kunabuka pamalo omwetsera mafuta appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください