Anthu awili m’boma la Balaka afa atadya zomwe iwo amaganizira kuti ndi chilazi. Anthu omwe afawa ndi bambo wazaka 50 ndi mwana wake wa zaka 17. Izi zadza pamene athuwa amadya zikhawo chifukwa chanjala kamba kakuti sadakolore chimanga chokwanira.. A Wongani Nyirenda omwe ndi ndi m’neri wa chipatala chachikulu cha Machinga atsimikiza ndipo ati bambo […]
The post Bambo ndi mwana afa atadya chilazi appeared first on Malawi 24.