Olira samugwira pakamwa ndipo mneneri wakale wa chipani chotsutsa cha DPP, a Nicholas Dausi, walira mokweza pa mwambo wa maliro wa a John Tembo. Poyankhula pa bwalo la za masewero la Dedza pamene amaimilira anzawo a Kondwani Nankhumwa amene ndi mtosgoleri otsutsa mu nyumba ya malamulo, A Dausi anati a Tembo anali katakwe pa ndale. […]
The post A Tembo anali munthu wabwino osati zochotsana muchipani akupanga a Mutharika – Dausi appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 