Palibe kopumira. Ngati a boma akuti mafuta akusowa chifukwa palibe ndalama za kunja, pompano aonjezekera kusowa chifukwa sipakhala owanyamula. Onse oyendetsa galimoto zikuluzikulu ati kuyambira pa 18 apa ayamba kunyanyala ntchito. Malinga ndi Malipoti, madalayivalawa ati ndi osakondwa kuti mavuto amene akhala akukumana nawo sanakonzedwe ndipo ena angoonjezekera. Mtsogoleri wa bungwe loyang’anira madalayivalawa a Mphatso […]
The post Samalani uko! A ma truck aopseza kuti anyanyalanso ntchito appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 