Tsitsani fizi ana abwelere kusukulu — watero mphunzitsi wa pa Mzuni

Mphunzitsi wina wa pa sukulu ya ukachenjede ya Mzuzu wauza oyendetsa sukuluyi kuti atsitse fizi kuti ophunzira apasukuluyi abwelere kusuluku. Mphunzitsiyu Dr Mariseni Mwale wanena izi kudzera pa tsamba lake la Fesibuku. “Pa Mzuni ingotsitsani fees yo ana abwerere kusuluku. Kuno kumabhowa,” Izi ndizomwe mphunzitsi wapasukulu ya ukachenjedeyi walemba. Sukulu ya ukachenjedeyi idatsekedwa mwezi watha […]

The post Tsitsani fizi ana abwelere kusukulu — watero mphunzitsi wa pa Mzuni appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください