Magalimoto apachikidwa kaye: Mitengo ya mathalasipoti yakwera

… Limbe-Chilimba pano ndi K2,500 kuchoka pa K1,000 Kupsa pamwamba ndi pansi pomwe ngati chigumu: anthu omwe apachika kaye magalimoto awo chifukwa chakusowa kwa mafuta alibe kothawira kamba koti wa minibasi ndi njinga za kabaza wakweza mitengo ya mathalasipotu mwa asafuna asiye. Lero ndi tsiku lachinayi kusowa kwa mafuta a galimoto kutafika pa mponda chimera […]

The post Magalimoto apachikidwa kaye: Mitengo ya mathalasipoti yakwera appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください