Yawo ija angoni: fisi wapangidwa ndiwo ku Ntcheu

Sadyeka uja lero wadyeka: Angoni a ku Ndagoma m’boma la Ntcheu adodometsa gulu pomwe achita ndiwo fisi yemwe wakhala akuwathera mbuzi m’mudzimo. Izi ndi malingana ndi kanema ina yomwe anthu akugawana m’masamba a mchezo yomwe ikuwonetsa azibambo angapo akuwawura fisi yemwe anamupha m’bandakucha wa lolemba pa 2 October. Izi zachitika m’mudzi wa Ndagoma omwe uli […]

The post Yawo ija angoni: fisi wapangidwa ndiwo ku Ntcheu appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください