…yati ikuwunika kuti apange apilu kapena ituluke zikho zonse Timu ya mpira wa miyendo ya Mighty Mukuru Wanderers yati iwunikira kuti ipeze ngati omwe anapanga chigamulo chawo analawa nkalabongo kapena ayi, ndipo yati ikudziwa ma timu omwe akuluakulu omwe apanga chigamulochi amasapota. Izi ndi malingana ndi a Chancy Gondwe omwe ndi mlembi wankulu wa bodi […]
The post Amapanga chiganizocho kapena adaledzera? – yadabwa Wanderers appeared first on Malawi 24.