Ndalama zambiri ndimazipeza pa bizinezi ya iligo osati kuyimba – watelo Nepman

Anthu m’masamba anchezo akugawana kanema ya oyimba Napier ‘ Nepman’ Longwe yomwe anamasuka ndikuwulura kuti luso lothyakula nyimbo lomwe ali nalo silimubweretsera ndalama zoti angadyetse banja lake kuyelekeza ndi bizinezi ya iligo yomwe akuti amapanga. Nepman yemwe amakhala munzinda wa Blantyre, anayankhula izi pa 18 August chaka chino nkatikati mwa kucheza kwake mu pologalamu ya […]

The post Ndalama zambiri ndimazipeza pa bizinezi ya iligo osati kuyimba – watelo Nepman appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください