Ochita kabaza ku Salima asimba lokoma

Anthu ochita kabaza wanjinga zamoto m’boma la Salima, tsopano akhala akusimba lokoma pamene bungwe loona za pamsewu la Directorate of Road Traffic and Safety Servies likhale likupereka ziphaso zoyendera pamsewu za ochita kabazawa. Poyankhulana ndi Malawi24, ena mwaochita kabazayu ati iwo ndiwosangalala kamba kaganizoli chifukwa zithandiza kuti apeze chiphaso choyendera pamsewu mosavuta. M’modzi mwawogwira ntchito […]

The post Ochita kabaza ku Salima asimba lokoma appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください