Wagwa mpesa; chinkulirano chabuka ku SDA yakum’mwera

Maranatha! chikondi cha pa abale chipitililebe: mpungwepungwe wabuka mumpingo wa Seventh Day Adventist pomwe akuluakulu a mchigawo chakumwera alavula nthambi ya Bangwe kuti simbaliso imodzi ya mpingowu ponena kuti ikuchita kusaweruzika. Izi ndi malingana ndi chikalata chomwe akuluakulu a mpingo wa SDA mchigawo chakummwera atulutsa pa 22 September, 2023 chomwe wasayinira ndi mtsogoleri wa mpingowu […]

The post Wagwa mpesa; chinkulirano chabuka ku SDA yakum’mwera appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください