Zipani za United Democratic Front (UDF) ndi UTM zadandaula kuti chipani cha Malawi Congress Party (MCP) chimapereka thumba la ufa lolemera 25 kilogalamu komanso ndalama kwa anthu omwe aponye voti pachisankho chachibwereza pa 26 September chosankha khansala ku Ntiya Ward mu Mzinda wa Zomba zomwe akuti ndizoletsedwa pamalamulo achisankho. Mlembi wamkulu wachipani cha UDF Abubaker […]
The post UDF ndi UTM zati MCP yapereka ndalama ndi ufa kwa anthu odzaponya voti appeared first on Malawi 24.