Ntchito ya kalozera sikugwilizana ndi chisankho cha mu 2025 — Macra

Bungwe la Malawi Communications Regulatory Authority (Macra) latsindika kuti ntchito yomwe bungweli ikugwira poika zizindikiro komanso zikwangwani mu malo osiyanasiyana (National Addressing System) sikugwilizana ndi pang’ono pomwe ndi chisankho cha pulezidenti, aphungu akunyumba yamalamulo komanso ma khansala chomwe chikuyembekezeka kuchitika mdziko muno mu chaka Cha 2025. M’modzi mwa akuluakulu ku bungweli, a Burnet Namacha, ndiwo […]

The post Ntchito ya kalozera sikugwilizana ndi chisankho cha mu 2025 — Macra appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください