Kwatuluka zithunzi zam’nanu pa masamba anchezo zothyakulidwa muphika otchedwa Photolab; komatu zithunzi zina ukaziona munthu ukumapukusa mutu kuli kusamvetsa kuti nzanga uja ndi uyuyu? Atayela komaso kutchena mochititsa kaso. Photolab ndi apulikeshoni (application) ya mufuni yomwe anthu amayigwiritsa ntchito kukongoletsa zithunzi ndipo ili ndi zitakataka zamakono zomwe zadzetsa chimwemwe chodzadza tsaya kwa ogwiritsa ntchitowo. Zina […]
The post Photolab wayatsa moto pa Malawi appeared first on Malawi 24.