Mnyamata wa zaka 18 waphedwa ku Balaka

Apolisi ku Balaka akusaka anthu amene anapha mnyamata wa zaka 18, Gift Libuda, yemwe anali mu folomu 3 pa sukulu ya St Charles Lwangwa Secondary. Malingana ndi mneneri wa Police m’bomali a Gladson M’bumpha, mnyamatayu anachoka kwawo lamulungu pa 10 September, 2023. Iye anapita kwa agogo ake kwa Chiyendausiku kuti akatenge katundu wina pokonzekela kutsegulira […]

The post Mnyamata wa zaka 18 waphedwa ku Balaka appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください