Bambo ali mchitokosi pa mulandu ogwirilira mwana wa zaka 8

Apolisi m’boma la Balaka amanga bambo wina, a Goodson Ali, a zaka 18 powaganizira kuti adagwirilira mwana wa zaka zisanu ndi zitatu (8). Malingana ndi wachiwiri kwa mneneri wa polisi ya Balaka, Mphatso Munthali, bamboyu adachita izi pa 2 September, 2023 m’mudzi mwa Kambadi m’boma lomweli la Balaka. A Munthali adati bambo oganizilidwayu akuti adapempha […]

The post Bambo ali mchitokosi pa mulandu ogwirilira mwana wa zaka 8 appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください