Bambo wadzikhwezera mkachisi

Bambo wa zaka 45 m’boma la Thyolo wadzipha podzimangilira mkachisi kamba koti nkazi wake anapeleka ku kachisiko ndalama yose yomwe anapeza atagwira ganyu. Nkhaniyi watsimikiza ndi mneneli wapolisi ya Masambanjati m’bomali, a George Kaleso, omwe azindikira mkuluyu ngati a Rex Kondwani omwe anali ochokera m’mudzi mwa Muwalo mfumu yaikulu Changata ku Thyolo komko. A Kaleso […]

The post Bambo wadzikhwezera mkachisi appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください