A Alick Saini omwe amatsogolera achinyamata a UTM ku Kasungu awamanga chifukwa choluma mphuno ya yemwe amatsogolera a chinyamata a chipani cha MCP ku Kasungu komweko. Apolisi ati nkhaniyi yachitika lachisanu usiku ku Kasunguko. Mneneri wa a polisi ku Kasungu, a Joseph Kachikho, ati awiriwa akuti adakumana pa malo ena omwera mowa. Ali pamalo omwewa […]
The post Wachinyamata wa UTM waluma mphuno ya mtsogoleri wa MCP ku Kasungu appeared first on Malawi24.