Mkulu wina m’boma la Mulanje waona mbonawona atakanilira panyumba yomwe anapita kuti akabe katundu m’bandakucha walero. Izi ndi malingana ndi kanema yemwe anthu akugawana m’masamba anchezo yemwe akuonetsa mkuluyu atavala kabudula wankati yekha atakanilira pa nyumbayi. Malipoti osatsimikizika akusonyeza kuti m’bandakucha wa lero, tsizina mtoleyu yemwe dzina lake silinadziwike, anapita ku nyumba ina m’boma la […]
The post Bambo wakanilira atapita kokaba appeared first on Malawi24.