Bungwe lowona za mphamvu zamagetsi la Malawi Energy Regulatory Authority (MERA), lalengeza kuti kuyambira lero mtengo wa magetsi wakwera kuyambira lero pa 1 September, 2023. Izi zadziwika pomwe bungweli lero linachititsa msonkhano wa atolankhani munzinda wa Lilongwe komwe amafotokoza za mtengo watsopano wa magetsiwu. Malingana ndi mkulu wa bungwe la MERA a Henry Kachaje, kwa […]
The post Mtengo wa magetsi wakwera appeared first on Malawi24.