M’modzi wa makomishonala a bungwe lomwe limawona zachisankho m’dziko muno la Malawi Electoral Commission (MEC) a Caroline Mfune apempha anthu a mdera la Ntiya Ward mu Mzinda wa Zomba kuti adzaponye voti yosankha Khansala wa kumtima kwawo pachisankho chomwe chikuyembekezeka kudzachitika pa 26 September chaka chino. A Mfune adayankhula izi mu Mzinda wa Zomba pomwe […]
The post MEC yalimbikitsa anthu a Ntiya Ward kuti adzaponye voti appeared first on Malawi24.