Bambo wa zaka 27 m’boma la Karonga wadabwitsa anthu pomwe wadula mutu wa nkazi komaso mwana wake kenakaso naye nkudzimangilira. Izi ndi malingana ofalitsa nkhani pa polisi ya Karonga a George Mulewa omwe azindikira bamboyu ngati Jonathan Mzumara omwe apha nkazi wawo Mervis Kumwenda komaso mwana wawo Ian Mzumara. A Mulewa ati nkhaniyi yachitika kumayambiliro […]
The post Zina ukamva: Bambo adula mutu wa nkazi ndi mwana kenaka nkudzikhweza appeared first on Malawi24.