Anthu m’masamba anchezo akulavulira zakukhosi chipani chotsutsa cha DPP pa malipoti oti chinakana kuthandiza membala wake yemwe wamwalira atadwala ku mwambo oyika m’manda malemu Goodall Gondwe. Malipoti akuti DPP inakananso kunyamula thupi lake, ati poti analibe udindo ku chipani. Tsamba lino lamvetsedwa kuti m’modzi mwa akafa ndikhale a chipani cha DPP, Criff Ngomango, anadandaula kuti […]
The post DPP ikudzudzulidwa polephera kusamala maliro a membala wake appeared first on Malawi24.
Moni Malawi 