Apolisi m’boma la Dowa a njata anthu khumi ndi m’modzi (11) kaamba kogulira mafuta a galimoto m’zigubu. Watsimikiza za nkhaniyi ndi ofalitsa nkhani pa polisi ya Dowa a Alice Sitima omwe afotokoza kuti anthuwa amangidwa kumathero asabatayi m’bomali. A Sitima ati a polisi m’bomali anakhazikitsa chipikisheni m’madera ena m’bomali ndipo apa ndipamene anakumanizana ndi anthuwa […]
The post Anjatwa kaamba kogulira mafuta galimoto m’zigubu appeared first on Malawi24.