Apolisi lero alanda zigubu zoposa 100 komanso mabotolo omwe anthu amafuna kuguliramo mafuta a galimoto ku Lilongwe. Mneneri wa polisi ya Lilongwe a Hastings Chigalu ati apolisi alanda zigubuzi atayendera malo othirira mafuta a galimoto. A Chigalu ati a polisi akufuna kuthana ndi mchitidwe wogula mafutawa ndi kumakagulitsa pa mtengo wokwera. Lachiwiri sabata lino bungwe […]
The post Apolisi alanda zigubu ku Lilongwe appeared first on Malawi24.