Pamene dziko lino likuvutika pa nkhani ya zachuma, phungu wa nyumba ya malamulo wa dera la kum’mwera kwa boma la Chitipa a Werani Chilenga, ati akufuna kuti nyumba ya malamulo ikambirane zoti aphungu opuma azilandira malipiro a pamwezi kwa moyo wawo onse. Izi ndi malingana ndi chikalata cha a Chilenga chomwe chikuzungulira m’masamba a mchezo […]
The post Phungu opuma azilandira ndalama moyo wawo onse – watelo Chilenga appeared first on Malawi24.
Moni Malawi 