Australia imathamanga kwambiri — watero Mwai Kumwenda

Wosewera kutsogolo kwa timu ya mpira wa manja ya Malawi Mwai Kumwenda wati timu ya Australia, yomwe yagonjetsa Malawi lero mu mpikisano wa dziko lonse lapansi wa Netball World Cup, imathamanga kwambiri. Kumwenda amayankhula izi lero pakutha pa masewero a pakati pa Malawi ndi Australia omwe Malawi yaluza ndi zigoli 70 kwa 46. Chiyambireni, Malawi […]

The post Australia imathamanga kwambiri — watero Mwai Kumwenda appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください