Oyimba yemwe ali m’dziko la America Alberto Fernando Zacharias yemwe amadziwika ndi dzina loti Jolly Bro mwachidule JB, wayankha za galimoto yomwe Tay Grin wapatsidwa ponena kuti iye samadalira zinthu zopatsidwa. Izi zikudza kutsatira zomwe yachita imodzi mwa makampani obwereketsa magalimoto mdziko muno ya Diplomats Car Hire yomwe lachitatu sabata yatha yapereka galimoto yatsopano ya […]
The post Ine zinthu zopatsidwa ayi – watelo JB poyankha za galimoto yomwe Tay Grin wapatsidwa appeared first on Malawi24.