Mthengo mudalaka njoka: De Jongh akulingalira zobanduka

Mphunzitsi wa mkulu wa timu ya Silver Strikers, Hendrikus Pieter de Jong yemwe ndiochokera m’dziko la Netherlands wati akuona kuti mpira wa ku Malawi wamulaka ndipo wati akuganiza kuti apite dziko lina. De Jongh wayankhula izi dzulo pakutha pa masewero omwe timu yake ya Silver Strikers yagonja ndi chigoli chimodzi kwa chilowere ndi timu ya […]

The post Mthengo mudalaka njoka: De Jongh akulingalira zobanduka appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください