Bwalo loweluza milandu m’boma la Balaka lalamula kuti bambo wina wa zaka 37 zakubadwa, a Frazer Satha omwe ndi sing’anga wa zitsamba, alipile chindapusa cha ndalama zokwana K90,000 apo bii akagwire ntchito ya kalavulagaga ku ndende kwa miyezi khumi ndi isanu (15) atawapeza olakwa pa mlandu opeza ndalama mwa chinyengo. Oyimira boma pa milandu a […]
The post Sing’anga alipilitsidwa chindapusa atakanika kudzutsa munthu omwalira appeared first on Malawi24.
Moni Malawi 
