Mwalephera, tisankhe atsogoleri ena chaka chino – atelo mamembala a NGC ya DPP

…ati NGC siyinasankhe a Mutharika Mamembala ena akomiti yayikulu ya chipani cha DPP (NGC) akupitilira kuwulura zakutsimba ndipo ati mtsogoleri wawo Peter Mutharika walephera kuyendetsa bwino chipanichi choncho sakuyenera kudzionjezera nthawi yolamulira. Izi ndi malingana a Baxtor Kita omwe mogwilizana ndi a Werani Chilenga komaso a Simeon Phiri, anachititsa msonkhano wa atolankhani Lolemba mumzinda wa […]

The post Mwalephera, tisankhe atsogoleri ena chaka chino – atelo mamembala a NGC ya DPP appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください