…wati ziphona zinkafuna kubilibinya Ken Nsonda ku msonkhanoko …wati DPP ikufuna kubweretsa ma khadi kwa mamembala Madzi akupitilira kuchita katondo ku chipani cha DPP pomwe zadziwika kuti ku msonkhano wa National Governing Council omwe unalipo posachedwapa, ambiri achokako atakhumudwa ndipo akuti a Ken Nsonda ankafuna kupatsidwa mabwande ndi ziphona. Izi ndi malingana ndi ofalitsa nkhani […]
The post Anthu abwera atakhumudwa ku msonkhano wa NGC – watelo Dausi appeared first on Malawi24.
Moni Malawi 