Ku-Li-mbuli?: Siine mbava, aphwanya poti n’nawaletsa kupha wakuba – walira mwini loji ku Mulanje

…wati katundu wa ndalama zoposa K700 miliyoni wawonongedwa A Edson Nachuma omwe ndi mwini wake wa malo ogona alendo omwe awotchedwa Lolemba a Edga’s ku Limbuli m’boma la Mulanje, akanitsitsa mwantu wa galu kuti iwo ndi mbava komaso chigawenga chowopsa mdelari. Lolemba pa 26 June, 2023, kunali chipwilikiti m’dera la Limbuli, m’boma la Mulanje pomwe […]

The post Ku-Li-mbuli?: Siine mbava, aphwanya poti n’nawaletsa kupha wakuba – walira mwini loji ku Mulanje appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください